Monga pali bambo, mayi ndi ana awo mu banja padziko lapansi,ndiponso pali Atate Akumwamba, Amai akumwamba, ndi ana awo wakumwamba amene adzalandire gawu la chuma cha Mulungu mu Ufumu wa Kumwamba.
Monga momwe makolo padziko lapansi adziperekera ana awo, Makolo akumwamba nawonso amakhululukira ana awo machimo awo kudzera mu kudzipereka kwawo ndi chikondi chokhetsa mwazi pa mtanda, ndipo awalonjeza iwo chipulumutso.
Mamembala a Mpingo wa Mulungu akuyenda njira ya chikhulupiriro ndi kuyamika chisomo cha Makolo akumwamba, kutsatira mawu a Atate Khristu Ahnsahnghong mokondwera.
Komanso, tinali nao atate a thupi lathu akutilanga, ndipo tinawalemekeza; kodi sitidzagonjera Atate wa mizimu koposa nanga, ndi kukhala ndi moyo? Ahebri 12:9
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi