Ntchito yeniyeni ya mpingo ndikulalikira
uthenga wachipulumutso ku dziko lonse la pansi.
Pa Tsiku la Pentekoste, Mulungu adatsanulira Mzimu Woyera
pa Mpingo wa Mulungu womwe Petro ndi Yohane ankapitako
Zaka 2000 zapitazo - Mpingo womwe umasunga Sabata,
Paskha, ndi Pentekoste m’Chipangano Chatsopano.
Mu m'badwo wa Mzimu Woyera, nawonso, Mulungu watsanulira
Mzimu Woyera pa Mpingo wa Mulungu womwe uli ndi Chipangano Chatsopano
ndipo adapatsa Mpingo ntchito yopulumutsa dziko la pansi.
Komatu mudzalandira mphamvu, Mzimu Woyera atadza pa inu:
ndipo mudzakhala mboni zanga m'Yerusalemu,
ndi m'Yudeya lonse, ndi m'Samariya, ndi kufikira malekezero ake a dziko. Machitidwe 1:8
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi