Monga momwe Mulungu anamiza gulu lankhondo la Aigupto pa Nyanja Yofiira,
Iye anawononga mphamvu ya uchimo ndi kupatsa anthu chiyembekezo cha kuuka pa Tsiku la Kuuka kwa AKufa.
Ndilo tsiku limene Yesu mwiniyo anaonetsa kuti tidzasandulika
thupi lanyama kukhala thupi lauzimu.
Tsiku limene ankhondo a Aigupto anaikidwa m’manda m’Nyanja Yofiira
ndipo Aisrayeli anatera pa Nyanja Yofiira linali Lamlungu.
Choncho, kuti tizikumbukira tsikuli, Tsiku la Zipatso Zoyamba mu Chipangano Chakale
linakhazikitsidwa ndipo linkasungidwa nthawi zonse pa Sunday.
Mogwirizana ndi ulosiwu, Yesu Kristu anakhala chipatso choyambirira cha iwo
akugona ndipo anaukitsidwa kwa akufa Sunday.
Pakuti ufulu wathu uli Kumwamba;
kuchokera komwenso tilindirira Mpulumutsi, Ambuye Yesu Khristu;
amene adzasanduliza thupi lathu lopepulidwa, lifanane nalo thupi lake la ulemerero,
monga mwa machitidwe amene akhoza kudzigonjetsera nao zinthu zonse.
Afilipi 3:20-21
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi