Mu 1964,
Busan, South Korea
Kuchokera kumalekezero a dziko lapansi,
nyali ya choonadi inaunikira.
Pamene kuwala kwa moyo kunawala,
mdima unabwerera.
Ndipo kuwalako kunafalikira padziko lonse lapansi.
Kukhazikitsidwa kwa Mpingo wa Mulungu mu 1964
Kulalikira ku North America mu 1997
Kulalikira ku Asia mu 1997
Kulalikira ku South America mu 1998
Kulalikira ku Oceania mu 2002
Kulalikira ku Central America mu 2003
Kulalikira ku Africa mu 2004
Kulalikira ku Ulaya mu 2005
Kukondwelera kwa chaka cha 60 cha Mpingo wa Mulungu mu 2024
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi