“Kodi mamembala a Mpingo wa Mulungu anachita bwanji ntchito imeneyi mokondwera komanso mwachimwemwe?”
Mpingo wa Mulungu umasamalirana wina ndi mzake ngati banja limodzi, mosatengera mtundu kapena fuko. Kusamalirana kwawo ndi chikondi kuli pa anthu a m’mudzi wapadziko lonse lapansi.
Mpingo wa Mulungu umagwira ntchito za uvolontiya monga kusamalira za chilengedwe, Chithandizo chapangozi, kupereka magazi, thandizo Lapadera, ndi Masapota ochemelera masewero mopanda malire ndi mtima wa amayi komanso kuthandiza osowa.
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi