Moyo wa pa dziko lino umayendera limodzi ndi ngozi zadzidzidzi, matenda, ndi ngozi yosalekeza. Sitikuyenera kusiya Mulungu Ahnsahnghong amene amatiteteza ku zoopsa zonsezi kudzera mu Paska wa pangano latsopano; Tiyenera kukumbukira kuti ziphunzitso Zake zonse ndiwo mawu a chikondi cha Mulungu ndipo cholinga chake ndi kutengera ana Ake kumwamba, kotero ndikupereka mayamiko ndi matamando kwa Mulungu, amene wakhala Wamphamvu Wathu mu m’Ziyoni.
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi