Baibulo ndi buku la mawu a Mulungu.
M’buku la Genesis imalemba za ntchito yolenga ya Mulungu.
mu Genesis 1:26, pamene Mulungu analenga munthu, Iye anati, “Tipange munthu m'chifanizo chathu, monga mwa chikhalidwe chathu.”
Akatswiri a Baibulo amati mawu akuti, “ife” ndi chinsinsi chosathetsedwa.
Nchifukwa chiyani Mulungu sanati “ine” koma “ife”?
Baibulo loyamba la Chihebri limalemba Mulungu, amene amazitcha kuti “ife,” monga Elohim.
#GululaUtumikiwaDzikoLonselaMpingowaMulungu #Ahnsahnghong #MulunguAmai #MpingowaMulunguChoonaPlus #Baibulo #Elohim #Ife #MulunguOchuluka #MzimuNdiMkwatibwi #Moyo
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi