Yerusalemu Watsopano! Yerusalemu Watsopano!
Inu mwatsika kuchokera Kumwamba, O Amayi!
Ndi nsembe yaikulu ya Mulungu, kachisi wamangidwa.
Kuwala kwa ulemerero wa Mulungu kunawalira pa Yerusalemu ngati nyale.
Mitundu yonse idza kwa kuwala, bwerani ku kuwala Kwake.
Yerusalemu Watsopano, Mayi wathu!
Kwamuyaya, ulemerero Wanu udzawala!
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi