Pali mipingo yambiri padziko lapansi.
Kodi chikhalidwe cha mpingo umene Mulungu akuulamulira ndi chiyani?
Monga momwe kuli lamulo m’dziko lililonse ndipo mafumu amalamulira ndi lamulo limenelo, pali lamulo la pangano latsopano mu Mpingo wa Mulungu umene Mulungu, Mfumu ya kumwamba, akulamulira.
Ndiponso, mofanana ndi m’fanizo la phwando la ukwati wakumwamba, Mulungu Atate ndi Mulungu Amayi ayenera kukhalapo.
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi