Yesu anakhazikitsa Paska wa pangano latsopano ndi mkate ndi vinyo ndipo analamula kuti asungidwe. Ndipo oyera mtima onse a Mpingo woyamba, kuphatikizapo Petro, Yohane, ndi Mtumwi Paulo, amene Akhristu ambiri masiku ano amawalemekeza, anasunganso Paska wa Pangano Latsopano motsatira ziphunzitso Zake.
Ichi n’chifukwa chake mamembala a Mpingo wa Mulungu padziko lonse lapansi amasunga Paska.
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi