Popeza anthu sangazindikire chowonadi ndi chonama, amapita ku njira yolakwika.
Pachifukwa chimenechi, Yesu anawaphunzitsa kufufuza kumene kunachokera, kaya ndi kwa Mulungu kapena ayi.
Kupembedza kwa Lamlungu ndi Khrisimasi, zomwe anthu amasunga masiku ano, zidachokera ku kulambira kwa mulungu dzuwa pomwe tsiku la Sabata ndi Paskha, zomwe zimasungidwa mu Mpingo wa Mulungu, ndi zipatso za chowonadi chochokera kwa Mulungu.
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi