Nkhani za m’Baibulo zimasonyeza kuti Yesu anabadwa m’nyengo yofunda pamene nkhosa zinkadya msipu ngakhale usiku.
Mwambo wokondwerera kubadwa kwa Yesu pa December 25, umene suli panyengo yoyenerera ya kubadwa kwa Yesu, unachokera ku mapwando achiroma a mulungu dzuŵa. Mwambo umenewu unalowetsedwa mu mpingo pambuyo pa M’badwo wa Atumwi.
Mpingo wa Mulungu sumakondwerera Khirisimasi, pa December 25, monga kubadwa kwa Yesu potsatira ziphunzitso za m’Baibulo zoperekedwa ndi Khristu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi.
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi