Mtumwi Yohane analandira vumbulutso pa chisumbu cha Patmo ndipo anazindikira kuti Mulungu amalamulira chilengedwe chonse ndi anthu.
Anachitiranso umboni kuti mu mpingo umene Mulungu akulamulira payenera kukhala Mkazi wa Mwanawankhosa limodzi ndi ukwati wa Mwanawankhosa.
Mpingo wa Mulungu ndi mpingo umene Mwanawankhosa ndi Mkazi Wake, omwe ndi Khristu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi, akulamulira lero.
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi