Mulungu analola Paskha ngati njira yoti tigonjetse Satana.
Satana anayesa kuletsa kubadwa kwa Mose ndi Yesu kuti aletse mphamvu ya Mulungu ya Paskha.
Komabe, monga mmene anagonjetsedwera kumwamba pamene anatsutsa Mulungu, iye anagonjetsedwanso padziko lapansi pano.
Anthu osaŵerengeka padziko lapansi akukhamukira ku Ziyoni kumene Pasika wa pangano latsopano amachitirako.
Iyi ndi ntchito ya Khristu Ahnsahnghong ndi Mulungu Mayi amene amabweretsa chigonjetso chauzimu.
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi