Paska wa Pangano Latsopano amakondwereredwa chaka chilichonse ndi mamembala onse a mpingo wa Mulungu padziko lonse lapansi. Ili ndi tsiku laulemerero pamene amalandira thupi ndi mwazi wa Mulungu kuti akhale ana a Mulungu.
Pa Paskha, Khristu anapatsa ophunzira Ake mkate ndi vinyo monga thupi ndi mwazi Wake. Iye ananena kuti anthu amene amadya mkate ndi kumwa vinyo akhoza kukhala mamembala a m’banja lakumwamba amene amaitana Mulungu Atate ndi Amayi wawo, chifukwa alandira thupi ndi mwazi wa Mulungu.
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi