Mulungu mwiniwake ndiye anakhazikitsa Paska panthawi ya ulendo wa Aisraele, ndikulamula kuti, “Chitani ichi chaka chilichonse,” ndipo anaika akerubi kuti alondere njira yopita ku mtengo wa moyo m’munda wa Edeni. Popeza Mulungu yekha ndiye angatsegulenso njira yopita ku Paska, choonadi cha mtengo wa moyo, Yesu anabwera zaka 2,000 zapitazo, ndipo Khristu Ahnsahnghong anabwera masiku otsiriza.
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi