Pamene Mulungu anabwera padziko lapansi m’thupi, ndi dzina lakuti “Yesu,” malingana ndi ulosi, Aisraele a nthawi imeneyo ankakhulupirira Mulungu koma sanakhulupirire Yesu.
Nchimodzimodziso, ngakhale kuti Mulungu wabwera monga Mzimu Woyera ndi Mkwatibwi malingana ndi ulosi, anthu ambiri sakutsatira njira yopita ku ufumu wakumwamba monga momwe Khristu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi anaphunzitsira. M'malo mwake, akuchita chimodzimodzi monga amene anazunza Yesu, kumutcha Iye “wa mpatuko wa ku Nazareti.”**
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi