Ndikofunikira kukhala ndi mtima woyamika ngakhale m’nyengo zovuta.
Dziko lino ladzaza ndi kung’ung’udza ndi madandaulo chifukwa lilibe chiyembekezo cha kumwamba ndipo limangoyang'ana zinthu zapadziko lapansi zokha. Komabe, monga ana a Khristu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi, mamembala onse a Mpingo wa Mulungu ali ndi lonjezo la ufumu wosatha wakumwamba, zimene zimatithandiza kukhala ndi moyo woyamika.
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi