Amene amati, “Analonjeza kundipatsa chilichonse, koma sindinalandire,” amauzidwa kuti n'chifukwa chakuti sanayesetse kupempha, kapena anapemphera zofuna zawo. Timaphunzitsidwa kupemphera ndi chikhulupiriro m'chifuniro cha Khristu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amai, ogwira ntchito ya chipulumutso cha anthu, ndipo tiyenera kupempherera dziko ndi abale komanso alongo athu a ku Ziyoni.
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi