Mulungu akhoza kuchita chilichonse, ngakhalezinthu zimene anthu sangathe kuchita.Ngakhale Satana atayesetsa bwanji kulepheretsa uthenga wabwino pochititsa khungu maganizo a anthu, ntchito ya Mulungu siingathe kusokonezedwa monga momwe dziko lapansi silingaimitsidwe kuzungulira.
Tiyenera kuyamika Khristu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi omwe amatiteteza mpaka kumapeto ndikukhala ndi chikhulupiriro chakuti tidzapambana ngakhale satana atatilepheretsa.
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi