Masiku ano, ngakhale Mpingo wa Katolika, womwe umalambira pa Sunday, umavomereza kuti Sabata la m'Baibulo ndi Loweruka, osati Sunday.
Mu Chipangano Chakale, Yehova anati tsiku lachisanu ndi chiwiri ndi Sabata lake, nalamula kulisunga lopatulika monga lamulo la chinayi pa Malamulo Khumi. Mu Chipangano Chatsopano, Yesu ananenanso kuti Sabata lisungidwe mopatulika mpaka mapeto a nthawi.
Kulambira kwa Sunday, tsiku loyamba, komwe sikupezeka m'Baibulo, ndiko kuwonjezera kapena kuchotsa pa mawu a Mulungu, motero, kumabweretsa matsoka ndi kulepheretsa kulowa mu ufumu wa kumwamba.
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi