Mipingoyokhazikitsidwainapotozaulosi, “Taonani,adzandimitambo; ndipodiso lililonselidzampenyaIye,. . .” (Chivumbulutso 1:7) ndipoamakakamira kuti Khristu WobweraKachiwirisadzabweram ‘thupi koma adzawoneka ndi chochitikachauzimuchomwealiyense angathekuchitiraumboni.
Komabe,monga ulosi wa pa Yesaya 40:5 wakuti anthu onse adzaonaUlemerero wa Mulungu pa kudza kwakekoyamba sikutanthauzaKuti aliyense padzikolapansi adzachitiraumboni za Iye,Chivumbulutso 1:7 sizikutanthauzakutialiyensePadzikolapansi adzachitira umbonizaIye.
ZikutanthauzakutiIyeadzabweram ‘thupikuti aliyenseamuone.
Kulimbikirakwawo kukuwakakamizakutiasokoneze Baibulo, ndipoKumasulira Baibulo mwangozi kudzawatsogolera ku chiwonongekomongaanthuameneanakanaKhristu
pameneIyeanabwera monga Mpulumutsipakudza Kwake koyamba.
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi