M’masiku asanu ndi limodzi a Chilengedwe, Mulungu anapanga ziweto ndi nyama zakuthengo
ndipo analenga Adamu ndi Hava pomalizira pake pa tsiku lachisanu ndi chimodzi.
Uku kunali kuchitira umboni za kuloseredwa kwa Adamu ndi Hava—Mzimu ndi Mkwatibwi
amene adzaonekera mu nthawi ya Mzimu Woyera kuti apereke kwa anthu madzi a moyo.
Mpingo wa Mulungu umakhulupirira mwa Adamu wotsiriza,
Khristu Wobwera Kachiwiri Ahnsahnghong,
ndi Hava wotsiriza, Mulungu Amayi.
Komatu imfa inachita ufumu kuyambira kwa Adamu kufikira kwa Mose,
ngakhale pa iwonso amene sanachimwe monga machimwidwe ake a Adamu,
ndiye fanizo la wakudzayo.
Aroma 5:14
Ndipo mwamuna anamutcha dzina la mkazi wake, Heva;
chifukwa ndiye amake wa amoyo onse.
Genesis 3:20
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi