Kopulumukira wolakwa womangidwa pamzere wa imfa muzimu,
Ku dziko labwinja lodzala ndi zowawa za imfa,
Atate Akumwamba Ahnsahnghong
abwera ngati kuwala.
Atate athu
anabwera kuchokera Kummawa
Amayi anasiya mpando wachifumu Kumwamba, mpando wachifumu wa ulemerero mbuyo,
kufunafuna okondedwa Awo akuyendayenda mumdima.
Timapereka mayamiko amuyaya ndi matamando
kwa Atate Ahnsahnghong pakubwera padziko lapansi
ndi kutipulumutsa ife, ana Ake.
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi