Pamene wina anafunsa kuti, “Kodi ndichite chiyani kuti ndipeze moyo wosatha?” Yesu anayankha pogwiritsa ntchito Fanizo la Msamariya Wachifundo.
Anaphunzitsa kuti kusunga malamulo a Mulungu n’kofunika, koma chikondi n’chofunika kwambiri kuposa zimenezi.
Iye anatiuza kuti tisakhale ngati wansembe ndi Mlevi amene anaona munthu akufa m’njira atabedwa ndi achifwamba n’kungodutsa kumene, koma tikhale ngati Msamariya amene anamuchitira chisoni ndi kumuchitiranso chifundo.
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi