Monga momwe anthu amene anakhulupirira chiphunzitso cha geocentric kwa zaka pafupifupi 1,400 sakanatha kuvomereza heliocentrism, anthu akupatuka panjira ya chipulumutso chifukwa sakhulupirira chowonadi chonena za Mulungu Amayi, chimene Mulungu waphunzitsa anthu kudzera m’umboni wochuluka wa m’Baibulo.
Monga momwe madzi amazungulira ndi kulenjekedwa kwa dziko popanda kanthu, zimene zinalembedwa m’Baibulo zaka 3,500 zapitazo, ndi fundo zoona, umboni wa Baibulo wakuti Mulungu Amayi akutsogolera anthu kumwamba ndi woona. Ichi ndi chifukwa chake mamembala a Mpingo wa Mulungu padziko lonse lapansi amakhulupirira Mulungu Amayi.
Ndipo anati Mulungu, Tipange munthu m'chifanizo chathu, monga mwa chikhalidwe chathu,…Mulungu ndipo adalenga munthu m'chifanizo chake, m'chifanizo cha Mulungu adamlenga iye; adalenga iwo mwamuna ndi mkazi
Genesis 1:26-27
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi