Mulungu anasiya ulosi kwa
anthu onse amene akuvutika
ndi njala yauzimu ya
kumva mawu a Mulungu
akuti: “Idzanini kwa Mzimu
ndi Mkwatibwi ndipo
mulandire madzi a moyo.”
Pamene anthu onse apeza
Mzimu Woyera, Khristu Ahnsahnghong
ndi Mkwatibwi, Mulungu Amayi,
adzalandira madzi a moyo,
adzathetsa ludzu lawo
lauzimu, ndi kupulumutsidwa.
Ndipo Mzimu ndi mkwatibwi
anena, Idzani. Ndipo wakumva
anene, Idzani. Ndipo wakumva
ludzu adze; iye wofuna, atenge
madzi a moyo kwaulere.
Chivumbulutso 22:17
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi