Masiku ano, mipingo yambiri imalambira pa Sunday, koma ndi lamulo la anthu lokhazikitsidwa pamene Mfumu Constantine inalengeza Sunday kukhala tchuthi ndi tsiku la Kulambira mu AD 321.
Sabata lachisanu ndi chiwiri, limene Mulungu analonjeza madalitso ndi chiyero, ndipo anatilamula kulisunga mpaka mapeto a nthawi, ndi Loweruka.
Masiku ano, mpingo wokhawo umene umasunga Sabata Loweruka motsatira mawu a Mulungu ndi Gulu Lawumiki wa Dziko Lonse Mpingo wa Mulungu.
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi