O Amayi athu abwera kuchokera Kumwamba kudza padziko lapansi m'dzina la Amayi omwe ali chikondi, okhala ndi chikondi chosawerengeka monga nyenyezi zakuthambo, m'mafanizidwe aumunthu odzichepetsa.
Amayi athu ndiye kuunika, kuwala kwa ulemerero wa Mulungu mwini, ndi kasupe amene amatiyeretsa ku machimo athu onse ndi zodetsedwa; kasupe wa moyo!
O Amayi, Ufumu Wanu ukadzabwera, chonde titchule mayina athu, chonde titchule mayina athu!
Chonde lolani kuti tikhale nyenyezi Zanu zowala chikondi chanu chokongola kwanthawi za nthawi!
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi