Pali zinsinsi khumi ndi zitatu zamadalitso zomwe Amayi a Kumwamba aphunzitsa mamembala a banja lakumwamba: Kupereka chikondi ndi kukhala ndi moyo pamene akupereka ulemerero kwa Mulungu; kuyang'ana zinthu mokongola pamene tikugonjera kwa ena; kukukwilira chirichonse monga nyanja ndi maganizo a umwini; okhala nako kudzichepetsa ndi mzimu wakudzipereka, wakupirira zowawitsa za nthawi ino ndi mtima wamayamiko; kutumikirana wina ndi mzake kwinaku tikuyamikira ena.
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi