Pophunzira Baibulo, pali mfundo yofunika kuiganizira mwapadera. Ngati tiwerenga Chipangano Chakale pachokha, chimawoneka ngati chikutsutsana ndi Chipangano Chatsopano, ndipo tikamawerenga Chipangano Chatsopano, chimawoneka ngati chikutsutsana ndi Chipangano Chakale. Choncho, tikamawerenga Baibulo, choyamba tiyenera kumvetsetsa cholinga cha Chipangano Chakale ndi Chatsopano ndikukumbukira kusiyana pakati pa ziphunzitso za Chipangano Chakale ndi za Chipangano Chatsopano.
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi