Kwa ife, anthu, kuti tikhale ndi moyo, tiyenera kupuma, kudya, ndi kuchita masewera olimbitsa thupi. Momwemonso, mizimu yathu iyenera kupuma popemphera, kudya pophunzira mawu a Mulungu mwakhama, ndi kuchita masewera olimbitsa thupi polalikira mawu a Mulungu omwe tadya. Umu ndi momwe tingakhalire obadwanso monga anthu enieni akumwamba.
Alexander Wopambana anakweza molalo ya asilikali ake pakunena, “Ndidzagawananu mu tsogolo lanu.” Komabe, kale kwambiri kuposa Alexander Wopambana, Khristu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi, amene anabwera ku dziko lapansi monga Mzimu ndi Mkwatibwi, ananena mu Baibulo, “Ndidzakhala ndi inu. Musaope,” ndipo anatipempha kulalikira Uthenga Wabwino wa moyo ku dziko lonse ndi mtima wathu wonse ndi maganizo athu onse.
usaope, pakuti Ine ndili pamodzi ndi iwe;
usaopsedwe, pakuti Ine ndine Mulungu wako;
ndidzakulimbitsa; inde, ndidzakuthangata;
inde, ndidzakuchirikiza ndi dzanja
langa lamanja la chilungamo.
Yesaya 41:10
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi