Monga timafunikira zitsikimizo ndi ziphaso kuti tipeze zofunika pa dziko lapansi
Kotero tikufunika kukhala nzika za kumwamba -chitsimikizo cha Kumwamba
-kuti tikalowe Umufu wa Kumwamba. Baibulo limatiuza kuti chivomerezo
Choyenerera kulowa Kumwamba ndi Paskha Pangano Latsopano.
Monga momwe timakhulupirira m’dziko loonekali, tiyeneranso
Kukhulupilira m’dziko losaoneka. Nowa anakhulupirira mawu a
Mulungu pomwe Mulungu anati adzawononga dziko lapansi ndi mvula,
Zomwe anali asanakumanepo nazo. Mamembela a Mpingo woyambirira
Sanataye chiyembekezo cha kumwamba ngakhale mu mazunzo.
Tiyenera kukhulupirira mwa Mulungu Atate Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi amene anabwera monga Mzimu ndi Mkwatibwi mu m'badwo uno, ndi kusunga Paskha wa Pangano Latsopano malinga ndi lamulo la Mulungu. Tikatero titha kulandira ufulu wa kumwamba kudzera mu Pangano Latsopano Paskha, monga Mtumwi Paulo anachita.
Koma chikhulupiriro ndicho chikhazikitso cha zinthu zoyembekezeka,
chiyesero cha zinthu zosapenyeka.
Pakuti momwemo akulu anachitidwa umboni . . .
koma wopanda chikhulupiriro sikutheka kumkondweretsa . . . Ahebri 11:1–6
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi