M'buku la Ahebri, Khristu adaloseredwa kuti adzabweranso kudzapulumutsa anthu. Mika analosera kuti Mulungu adzabwera ku Ziyoni ndipo adzatiphunzitsanso njira zake masiku otsiriza. Yesaya analosera kuti yemwe amapatsa anthu moyo wosatha kudzera mu Paskha wa pangano latsopano ndi Mulungu wathu.
Khristu Ahnsahnghong anabweranso padziko lapansi mthupi kachiwiri ndipo anakhala Mfumu ya Ziyoni pobwezeretsa Paskha wa Pangano latsopano lomwe linathetsedwa mu AD 325. Atamaliza utumiki wake kwa zaka 37 malinga ndi ulosi wa mpando wachifumu wa mfumu Davide, anawaphunzitsa anthu a Ziyoni choonadi cha Mulungu Amayi, Mkwatibwi wa Mzimu.
Monga mmene Petro anazindikira Yesu kudzera poti Yesu anapereka mawu a moyo wosatha, Mpingo wa Mulungu umakhulupirira Khristu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi, amene akutipatsa mawu a moyo wosatha mu m'badwo wa Mzimu Woyera.
“Kubwera kwa Khristu kachiwiri ayenera kubwera mu dzina la Davide ndipo ayenera kumwalira atatha kulalikira Uthenga Wabwino kwa zaka 37.”
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi