Mwa ambiri amene anakumana ndi Yesu zaka 2,000 zapitazo,
Kenturiyo ndi mayi wa nthenda yotaya magazi
adalandira madalitso chifukwa adazindikira Yesu
monga mpulumutsi ndipo sanaphonye mwayi kudalitsidwa.
Kuti anthu onse okhala mu M’badwo wa Mzimu Woyera
kuti asaphonye mwayi kuti adalitsidwe, iwo ayenera kugwira ntchito
yapatsidwa ndi Mulungu mu Mpingo wa Mulungu, ndiye kuti mu Ziyoni
kumene Amayi Akumwamba amakhala
ndi chikhulupiriro chonse monga Petulo ndi Yohane.
“Bwerani, tsateni Ine ndipo ndidzakusandutsani asodzi a anthu.” Nthawi yomweyo anasiya makoka awo namutsata Iye. Mateyu 4:19–20
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi