Monga Mulungu Yehova mu M’badwo wa Atate, komanso monga Yesu Khristu mu M’badwo wa Mwana, komanso monga Mulungu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi-Mzimu ndi Mkwatibwi-M’badwo wa Mzimu Woyera, Mulungu amakhala chiyembekezo cha anthu mu Ziyoni, mzinda maphwando a Mulungu.
Mulungu Elohim ali ndi mphamvu zokhululukira machimo aanthu. Mpingo wa Mulungu, kumene Elohim Mulungu amakhala, ndi Ziyoni-malo omwe maphwando a Mulungu amakondwerera. Ndi Mpingo kumene kuli lonjezo lokhululukidwa machimo ndi ulemerero wa Ufumu wosatha wa Kumwamba.
“Idzani kuno kwa Ine nonsenu akulema ndi kuthodwa . . . ndipo mudzapeza mpumulo wa miyoyo yanu. Pakuti goli langa lili lofewa, ndi katundu wanga ali wopepuka.” Mateyu 11:28–30
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi