Wachifwamba wa kudzanja lamanja adadalitsidwa ndi chipulumutso
kudzera m’nzeru yosankha zinthu zomwe zili ndi phindu losatha
poyima ku mbali ya Yesu.
M’njira yathu ya chikhulupiriro popita Kumwamba, zinthu za phindu zomwe Mulungu
amavomereza ndizofunikira kuposa zinthu za phindu zomwe anthu amavomereza.
Monga m'mene Yesu adayitana ophunzira ake pafupi ndi Nyanja ya Galileya,
mu m'badwo uno, Khristu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi,
omwe ndi Mzimu ndi Mkwatibwi, akuyitana a ntchito
a Pangano Latsopano omwe adzasankhe phindu la Kumwamba.
Ndipo ananena, “Yesu, ndikumbukireni m'mene mulowa Ufumu wanu.”
Ndipo Iye (Yesu) ananena naye, “Indetu, ndinena ndi iwe,
Lero lino udzakhala ndine mu Paradaiso.” [Luka 23:42-43]
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi