Yesu amene anadza ku dziko lapansi nthawi yoyamba malinga ndi ulosi wa chifumu wa Davide anabatizidwa ali ndi zaka makumi atatu, ndipo analalikira Uthenga kwa zaka zitatu. Khristu Ahnsahnghong, amene anadza kachiwiri monga Davide wa uzimu, nayenso anabatizidwa ali ndi zaka makumi atatu ndi kukalalikira Uthenga kwa zaka makumi atatu zisanu ndi ziwiri zosalira, kukwaniritsa ulosi wa zaka makumi anayi.
Yesu Kristu ananeneratu kuti Mwana wa Munthu azabwera kachiwiri pamene mkuyu watsitsimuka, ndiye kuti, pamene Israyeli yalandila ufulu wodzilamulira mu 1948. Yemwe anabwera padziko lapansi lino kachiwiri monga Davide Wauzimu molingana ndi ulosiwu, kubwezeretsa maphwando a moyo amene anali atathetsedwa monga Sabata, Paskha, ndi ena., ndi kutsogolera anthu ku chipulumutso ndi Khristu Ahnsahnghong.
Mpingo wokhulupirira mwa Khristu Ahnsahnghong amene anabwera monga Davide ndi
Amayi Akumwamba amene Khristu Ahnsahnghong mwini yekha adachita umboni ndi Gulu la Utumiki
wa Dziko lapansi Mpingo wa Mulungu
koma adzamtumikira Yehova Mulungu wao,
ndi Davide mfumu yao, imene Ndidzawaukitsira. Yeremiya 30:9
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi