zaka zikwi ziwiri zapitazo, Yesu anakhululukira machimo
a anthu kudzera mu Paska wa Pangano Latsopano.
Popirira zowawa ndi masautso pa mtanda tsiku lotsatira,
limene linali Chikondwerero cha Mkate Wopanda Chotupitsa,
Yesu ananyamula machimo a ana Ake ndipo anasonyeza chikondi chake chachikulu pa iwo.
Njira ya chikhululukiro cha machimo athu yoperekedwa ndi Mulungu Ahnsahnghong,
amene anabweranso chifukwa cha chipulumutso cha anthu, ndi Amayi Akumwamba!
Mamembala a Mpingo wa Mulungu, amene avekedwa ndi chisomo cha chipulumutso kudzera mu chikondi cha Mulungu, tikusunga chikhulupiriro chathu ndi kuthokoza popanda kutaya chiyembekezo cha Kumwamba.
Umo chidaoneka chikondi cha Mulungu mwa ife,
kuti Mulungu anamtuma Mwana wake wobadwa yekha,
alowe m’dziko lapansi, kuti tikhale ndi moyo mwa Iye.
1 Yohane 4:9
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi