M'munda wa Edene, munali Mtengo wa kudziwitsa Zabwino ndi Zoipa, umene Mulungu anati, “Chifukwa tsiku lomwe udzadya umenewo udzafa ndithu," ndi Mtengo wa Moyo wopatsa moyo wosatha kwa yense wakudyamo. Komabe, Adamu ndi Hava anayesedwa ndi njoka sanamvere lamulo la Mulungu loletsa kudya chipatso choletsedwa., Zotsatila zake Sanalinso ololedwa kudya kuchokera ku Mtengo wa Moyo kotero anafa.
Choona Chenicheni cha Mtengo wa Moyo ndi Paskha wa Pangano Latsopano limene ife timadya thupi la Yesu ndi kumwa mwazi wake. Kuti atipulumutse ku uchimo wa kudya chipatso choletsedwa- uchimo woyenera imfa, Mulungu watipatsa mwayi umodzi woti tikhathe kusunga Paskha, kusunga m'mwezi wachiwiri malinga ndi kalendala wopatulika.
Paskha linathetsedwa mu AD 325, ndipo njira yopita ku Mtengo wa Moyo inatsekedwanso kachiwiri. Khristu Ahnsahnghong, woyambitsa Mpingo wa Mulungu, watsegula njira kachiwiri, monga mwa maulosi a m'Baibulo.
...phwando la vinyo wa pamitsokwe.. . . Iye wameza imfa kunthawi yonse . . . Ndipo adzanena tsiku limenelo, Taonani, uyu ndiye Mulungu wathu... Yesaya 25:6–9
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi