Pamene ana a Israele sanasunge malembo a Mulungu ndi malamulo,
Mulungu anawasiya ndipo anakhala mtundu ofooka oponderezedwa ndi amitundu.
Komabe, pamene mokhulupirika anatumikira Mulungu yekha,
Mulungu anali nawo nthawi zonse, ndipo anakhala mtundu wamphamvu ndi anali pa mtendere.
Monga kwalembedwa mu Oweruza, 1 Mbiri 1 Mafumu,
nthawi zonse akachita zoipa ndikusiya Mulungu,
sanakachitira mwina koma kugwa.
Pakuti zonse zinalembedwa kale zinalembedwa kutilangiza Aroma 15:4
Malinga ndi ziphunzitso za Baibulo, mpingo wa Mulungu umatsatira ziphunzitso za Mulungu Atate ndi Mulungu Amayi amene anabwera monga mpulumutsi mu M'badwo wa Mzimu Woyera.
Kotero Mulungu ali nafe nthaŵi zonse ndi kuteteza Ziyoni padziko lonse.
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi