Anthu onse, obadwa padziko lapansi, anaikika kumva zowawa za imfa ndi chilango cha gahena chifukwa cha machimo awo aimfa mu Ufumu wa Kumwamba.Nthawi zonse tiyenera kuyenda m’njira yachikhulupiriro ndi chiyamiko kwa Mulungu chifukwa chakumva zowawa pa mtanda kuti atipulumutse.
Mamembala a mpingo wa Mulungu amayetsetsa kukhala moyo wachiyamiko,
Pophunzira maphunziro kwa Aisrayeli amene anaonongedwa chifukwa chakuwilingula kwa Mulungu ataiwala mphammvu za Mulungu ndi chisomo chopulumutsidwa mu ukapolo wa zaka 400.
Koma zinthu izi zinachitika, zikhale zotichenjeza ife, kuti tisalakalake zoipa ife, monganso iwowo analakalaka… Koma izi zinachitika kwa iwowa monga zotichenjeza, ndipo zinalembedwa kutichenjeza ife, amene matsirizidwe a nthawi ya pansi pano adafika pa ife. Chifukwa chake iye wakuyesa kuti ali chilili, ayang'anire kuti angagwe.
1 Akorinto 10:6-12
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi