Msonkhano wa Misasa mu Chipangano Chakale, omwe umakumbukira mamangidwe a kachisi, ndi mthunzi, ndi zoona zake ndi Msokhano wa Misasa mu Chipangano Chatsopano, pomwe Mulungu amapereka Mzimu Woyera wa mvula yamasika monga madzi a moyo. Izi zikusonyeza kuti anthu onse ayenera kubwera kwa Mulungu Amayi, amene akuyimiridwa ngati Kachisi wa Yerusalemu , kotero kuti iwo akhoza kulandira Mzimu Woyera wa mvula yamasika ndi kupulumutsidwa.
Mulungu yekha angapereke madzi a moyo kwa anthu onse. Choncho, Mzimu ndi Mkwatibwi, amene kupereka madzi a moyo kwaulere mu masiku otsiriza, ndi Mulungu Atate ndi Mulungu Amayi.
Mzimu Woyera ndi mkwatibwi akuti, “Bwerani!” Ndipo amene akumva anena kuti Bwerani! Iye amene ali ndi ludzu abwere, ndipo aliyense amene afuna alandire mphatso yaulere ya madzi amoyo. Civumbulutso 22:17
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi