Pomwe Mose ndi Aisraeli ankamanga kachisi ngati malo oti Malamulo Khumi azikhalamo, pomvera chifuniro cha Mulungu, mitima ya anthu inasunthika ndipo mwachisangalalo adabweretsa mitundu yonse yazida zomaliza zomangira kachisi. Ichi chinakhala chiyambi cha Phwando la Misasa.
Yesu adasonkhanitsa zida zakachisi wa Kumwamba kudzera mukulalikira.
Tanthauzo lenileni la Phwando la Misasa la m’badwo uno ndikuti tipeze mamembala athu onse a m’banja la Kumwamba - zida za kachisi wauzimu, ndikuwatsogolera kwa Atate ndi Amayi, ndikumalizitsa kachisi wa Kumwamba.
“Mwa Iye chimango chonse cholumikizika pamodzi bwino, chikula, chikhale Kachisi wopatulika mwa Ambuye; chimene inunso mumangidwamo pamodzi, mukhale chokhalamo Mulungu mwa Mzimu.” Aefeso 2:21–22
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi