Mose atakweza manja ake pankhondo yolimbana ndi Aamaleki, ndikugawa Nyanja Yofiira ndi ndodo yake, komanso zomwe zinachitikira za njoka yamkuwa zonsezi zikuwonetsa kuti Mulungu nthawi zonse amakhala gwero la chipulumutso cha Aisraeli.
Monga ziwalo za Mpingo wa Mulungu alalikira uthenga wabwino, kudalira pa Mulungu Atate ndi Mulungu Amayi osadalira anthu, malo, kapena mkhalidwe, uthenga wabwino wachipulumutso wafalikira mwachangu ku dziko lonse lapansi.
‘‘Samalani kuopa kuti mungayiwale Yehova Mulungu wanu posasunga malamulo, zikhazikitso ndi malangizo ake amene ndikukupatsani lero.’’ Deuteronomo 8:11
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi