Monga Mulungu adadalitsa makolo akale achikhulupiriro ngati Abrahamu, Nowa, ndi Petulo pomwe adadalira mawu a Mulungu ngakhale munthawi zovuta, Amayang’ananso chikhulupiriro chathu pamavuto omwe timakumana nawo masiku anonso.
Mulungu Wamphamvuyonse adalenga dziko lapansi ndikuukitsanso akufa mwa mawu Ake. Tikadalira ndikumvera mawu a Mulungu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi, titha kuzindikira chisamaliro chodabwitsa cha Mulungu yemwe akutitsogolera ku chipulumutso mu Nthawi ya Mzimu Woyera.
“Pakuti maganizo anga sali maganizo anu, ngakhale njira zanu sizili njira zanga,”ati Yehova.”Monga kumwamba kuli kutali ndi dziko lapansi, momwemo njira zanga zili zazitali kupambana njira zanu, ndimaganizo angakupambana maganizo anu… momwemo adzakhala mau anga amene atuluka m’kamwa mwanga: sadzabwerera kwa Ine chabe, koma adzachita chimene ndifuna ndipo adzakula m’mene ndinawatumizira.”
Yesaya 55:8–11
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi