Solomoni, Gidiyoni, ndi Mose sanakana malamulo a Mulungu,
kunena kuti iwo sanali oyenerera kutsatira malamulo a Mulungu.
Komabe, Mulungu pakuona chikhulupiriro chawo chinali chosaoneka, ndipo anasankha iwo.
Mulungu anawapatsa mphamvu kuti agwire ntchiti yawo.
Chifukwa chomwe Mpingo wa Mulungu lokhazikitsidwa padziko lonse
ndi chakuti sitimayang’ana pa mphamvu zathu pamene tikugwira ntchito ya Mulungu
koma kukhulupilira mu mphamvu ya Khristu Ahnsahnghong ndi Amayi Akumwamba.
Zonse zinali chifukwa anadalira pa Iwo ndi kupita patsogolo.
Ndikhoza kuchita zonse kudzera mwa Iye amene amandipatsa mphamvu. Afilipi 4:13
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi