Mu M’badwo wa Mzimu Woyera, tiyenera kukhulupilira mwa Mulungu Atate ndi Mulungu Amayi ndi kutsatira mawu awo. Pokhapo ndi pomwe tingalandire cholowa cha kumwamba cha muyaya chomwe Mulungu watilonjeza.
Mamembala a Mpingo wa Mulungu amakhulupirira malonjezo a Mulungu ndipo amayenda mu njira ya uthenga wabwino, monganso Yoswa ndi Kalebi adakhulupirira lonjezo la Mulungu, osayang’ana zomwe zinali patsogolo pawo, monganso abwenzi atatu a Danieli sanachite mantha konse ngakhale adaopsezedwa ndi ng’anjo yamoto, ndipo monga momwe Nowa adamvera Mulungu ndi chikhulupiriro pomwe adamuuza zomwe sanazionepo kale.
Ndipo popanda chikhulupiriro nʼkosatheka kukondweretsa Mulungu, chifukwa aliyense amene amabwera kwa Iye ayenera kukhulupirira kuti Mulungu alipodi ndi kuti Iye amapereka mphotho kwa amene akumufunitsitsa. Ahebri 11:6
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi