Monga momwe Yesu adadzilolera kuti amugwire kuti akwaniritse uneneri wa m'Baibulo, mawu onse mBaibulo amakwaniritsidwa popanda uneneri uliwonse kusowa.
Uthenga wabwino wa Pangano Latsopano womwe Khristu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi anatilamula ife ukufalikira kudziko lonse lapansi kudzera mu Mpingo wa Mulungu monga ananenera mu Baibulo. Pokhapokha tili ndi chikhulupiriro choona ndi cholinga kukwaniritsa uneneriwu,
tidzatha kukwaniritsa ntchito zodabwitsa za Mzimu Woyera mu vuto lililonse.
Tsono ifenso tili ndi mawu a uneneri amene ndi odalirika kwambiri ndipo inu mudzachita bwino mukawasamalira mawuwa, monga kuwunika kumene kukuwala mu mdima, mpaka tsiku lidzayambe kucha, pamene nthanda idzayambe kuwala mʼmitima mwanu. 2 Petro 1:19
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi