Monga agalu, ntchentche, komanso anthu ali ndi nthawi ya moyo wawo,
ntchito ya chiwombolo cha Mulungu ilinso ndi nthawi yake yoikika komanso malire.
Mulungu adagawa ntchito ya chiombolo mu mibadwo itatu —M’badwo wa Atate ndi Mwana ndi Mzimu Woyera, ndipo adagwiritsa ntchito dzina la Mpulumutsi mu m’badwo uliwonse.
Mu m’badwo wa Mzimu Woyera, chipulumutso chidzamalizidwa ndi dzina latsopano la Yesu. Chifukwa chake mamembala a Mpingo a Mulungu, mboni mu m’badwo uno, amapemphera ndi kuyimba matamando mu dzina la khristu Ahnsahnghong, yemwe adabwera padziko lapansi molingana ndi maulosi a Baibulo.
“Iye amene adzapambane . . . Pa iye ndidzalemba dzina la Mulungu wanga ndi dzina la mzinda wa Mulungu wanga, Yerusalemu watsopano . . . dzina langa latsopano.” [Cibvumbulutso 3:12]
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi